Posts

Showing posts from January, 2025

Dziko Lonse Likulira: Papa Francis Wamwalira

Image
Lero dziko lonse likulirira. Mtumiki wathu, mtumwi wa mtendere, mtsogoleri wa Tchalitchi cha Katolika Papa Francis   wamwalira ali ndi zaka 88 . Nkhaniyi yatsimikizidwa ndi Vatican m'mawa uno, ndipo ikufalikira mofulumira padziko lonse lapansi. Papa Francis  Papa Francis, anabadwa ngati Jorge Mario Bergoglio ku Argentina, anali Papa woyamba kuchokera ku America, komanso wa mtundu wa Jesuit. Kuyambira atasankhidwa mu March 2013 , anasankha dzina Francis osati chifukwa chokopa, koma kuti akhale ngati Mtumiki wa osauka St. Francis of Assisi . Sanali Papa wa mphamvu anali Papa wa mtima . Anakana kukhala m'nyumba zokongola za Vatican, ndipo anasankha kukhala m'chipinda chaching'ono chisonyezo cha moyo wake wopanda kudzikuza. Papa Francis anali wolimba mtima. Anayankhula za kusintha kwa nyengo (climate change), kusasiyana kwa olemera ndi osauka, kulandira othawa kwawo, komanso za chikondi cha Mulungu kwa aliyense – ngakhale amene ena amawawona ngati osayenera. Anati: “...

PAUL KAGAME TO FIGHT BACK SOUTH AFRICA

Image
Rwandan President Paul Kagame says Rwanda is prepared for a confrontation with South Africa if necessary. This follows South African President Cyril Ramaphosa’s claim that M23 rebels and Rwanda’s defence force were responsible for the deaths of 13 South African soldiers in the Democratic Republic of Congo (DRC). Kagame says Ramaphosa had not warned Rwanda about its military activities in the DRC but instead requested logistical support while acknowledging South Africa’s efforts for peace. Kagame asserted that South Africa is not in a position to act as a peacemaker or mediator and warned that if South Africa seeks confrontation, Rwanda will respond accordingly. Kagame clarified details of his recent conversations with Ramaphosa, stating, “What has been said about these conversations in the media by South African officials and President Ramaphosa himself contains a lot of distortion, deliberate attacks, and even lies." "If words can change so much from a conversation to a publ...

MA ARV AYAMBA KUSOWA MU MALAWI

Anthu pafupifupi 1 million (936,480) mdziko muno ali pachiopsezo chosowa mankhwala otalikitsa moyo a ma ARV ngati dziko la America lipitilire ndi ganizo losiya kupereka thandizo lomwe limadzera Ku bungwe la Presidents Emergency Plan for Aids Relief (PEPFAR). Izi ndimalinga ndi zomwe lanena bungwe la amFAR lomwe limapanga kafukufuku komanso kuthandizira ntchito zolimbana ndi matenda a AIDS komanso kachirombo ka HIV. Malinga ndi lipotili Malawi ndi dziko limodzi lomwe likhudzidwe pa anthu opyora 20 million pa dziko lonse omwe amapindura ndi thandizo la Ma ARV kudzera mu PEPFAR. President Donald Trump wa dziko la America analamula kuti mabungwe adzikolo omwe akugwira ntchito zachifundo mayiko ena asiye kaye kugwira ntchito kwa miyezi itatu.

A 3 YEAR OLD CHILD HAVE DROWN

 A 3-year-old boy child has  drowned in a stagnant water in Balaka, Malawi. Balaka Police Public Relations Officer Gladson M'bumpha said the incident took place on Tuesday, January 28, 2025 at Kapire Village in Traditional Authority Nsamala in Balaka, Malawi. M'bumpha identified the child as Happy Loti who went to the neighbour's house to play with his friends. "The child entered in the neighbours house but within a short period of time, the deceased went out from the house and he did not return until his friends followed him, but found him lying dead in a stagnant water very close to the house" Said M'bumpha  Balaka District Hospital postmortem examination conducted by the medical practitioner confirmed that the cause of death was due to suffocation, secondary to drowning. The police is therefore arging the parents to monitor their children whenever they are going to other errands.

DR LAZARUS CHAKWERA ASSENTED THE BILLS

 President Lazarus Chakwera has assented to nine bills which were passed by Parliament. The bills are  Bill No. 22 of 2024: Constitution (Amendment). Bill No. 23 of 2024: Judicial Service Administration. Bill No. 25 of 2024: Financial Services (Amendment). Bill No. 26 of 2024: Insurance. Bill No. 27 of 2024: Public Procurement and Disposal of Public Assets. Bill No. 30 of 2024: Value Added Tax (Amendment). Bill No. 31 of 2024: European Investment Bank (Water Energy Framework) Loan (Authorisation).  Bill No. 32 of 2024: OPEC Fund for International Development (Shire Valley Transformation Programme Phase II) Authorisation and Ratification). Bill No. 33 of 2024: Appropriation (Amendment). This is in line to exercise of the powers vested in him by Section 89 of the Constitution. State house Press Secretary Anthony Kasunda has confirmed. “I can confirm that His Excellency has assented to all the Bills which were presented to him by the Office of the Speaker,” Kasunda said.

KWAPEZEKA BOKOSI YODWABWISA KU NDIRANDE

 Banja lina ku Ndirande mu mzinda wa Blantyre ladzidzimuka lero mmawa litapeza bokosi la maliro pa chipata cholowera kunyumba kwao. Banjalo linaitana amfumu komanso apolisi omwe analamula kuti atsegule kuti awone zomwe zili mkatimo. Anthuwo atatsegula, angopezamo nsalu. Pakadali pano, kafukufuku ali mkati kuti apeze yemwe wasiya bokosilo pamalopo komanso cholinga chake.
 Welcome! Mandala will be publishing news stories that have just happen in the world.

Popular posts from this blog

Mfumu Yaikulu Gawa Undi Aletsa Magule Opanda Ulemu pa Kulamba 2025

Ngozi ya Sitima ya M'madzi ku Likoma: Atatu afa, ena asanu ndi atatu apulumutsidwa

Nkhani Yachisoni ku Mchinji: Bambo wamangidwa Atapha Mwana Wake Chifukwa Chosamvera